Maliko 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Herode anali kulemekeza+ Yohane, pakuti anali kumudziwa kuti ndi munthu wolungama ndi woyera,+ choncho anali kumusunga bwino. Atamva+ zonena zake anathedwa nzeru, komabe anapitiriza kumumvetsera mokondwa.
20 Herode anali kulemekeza+ Yohane, pakuti anali kumudziwa kuti ndi munthu wolungama ndi woyera,+ choncho anali kumusunga bwino. Atamva+ zonena zake anathedwa nzeru, komabe anapitiriza kumumvetsera mokondwa.