-
Yohane 19:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Choncho pamene Pilato anamva mawu amenewa, anatulutsa Yesu panja, ndipo iye anakhala pampando woweruzira milandu, pamalo otchedwa Bwalo Lamiyala, koma pa Chiheberi otchedwa Gabʹba·tha.
-
-
Machitidwe 12:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Koma pa tsiku loikidwiratu, Herode anavala zovala zake zachifumu ndi kukhala pampando wake woweruzira milandu, ndi kuyamba kulankhula nawo.
-
-
Machitidwe 25:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Choncho onse atafika kuno, sindinachedwe, koma tsiku lotsatira ndinakhala pampando woweruzira milandu ndi kuitanitsa munthuyo kuti abwere naye.
-