Yohane 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano anthu okhala naye pafupi ndi anthu ena amene m’mbuyomo anali kumuona akupemphapempha anayamba kunena kuti: “Si uyu kodi amene anali kukhala pansi n’kumapemphapempha uja?”+
8 Tsopano anthu okhala naye pafupi ndi anthu ena amene m’mbuyomo anali kumuona akupemphapempha anayamba kunena kuti: “Si uyu kodi amene anali kukhala pansi n’kumapemphapempha uja?”+