Machitidwe 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho Paulo anaimirira, ndipo anakweza dzanja+ lake ndi kunena kuti: “Anthu inu, Aisiraeli, ndi ena nonse oopa Mulungu, tamverani.+
16 Choncho Paulo anaimirira, ndipo anakweza dzanja+ lake ndi kunena kuti: “Anthu inu, Aisiraeli, ndi ena nonse oopa Mulungu, tamverani.+