1 Mafumu 17:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako Yehova anamva mawu a Eliya,+ moti moyo wa mwanayo unabwerera mwa iye, ndipo anakhala wamoyo.+ 2 Mafumu 4:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Anayambanso kuyenda uku ndi uku m’nyumbamo. Atatero anapitanso kukaweramira mwanayo. Pamenepo mwanayo anayamba kuyetsemula mpaka maulendo 7, kenako anapenya.+ Aheberi 11:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Akazi analandira akufa awo amene anauka kwa akufa.+ Koma anthu ena anazunzidwa chifukwa sanalole kusiya chikhulupiriro chawo kuti amasulidwe. Iwo anachita zimenezi kuti adzauke kwa akufa, komwe ndi kuuka kwabwino kwambiri.
22 Kenako Yehova anamva mawu a Eliya,+ moti moyo wa mwanayo unabwerera mwa iye, ndipo anakhala wamoyo.+
35 Anayambanso kuyenda uku ndi uku m’nyumbamo. Atatero anapitanso kukaweramira mwanayo. Pamenepo mwanayo anayamba kuyetsemula mpaka maulendo 7, kenako anapenya.+
35 Akazi analandira akufa awo amene anauka kwa akufa.+ Koma anthu ena anazunzidwa chifukwa sanalole kusiya chikhulupiriro chawo kuti amasulidwe. Iwo anachita zimenezi kuti adzauke kwa akufa, komwe ndi kuuka kwabwino kwambiri.