Luka 1:77 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 77 Kukadziwitsa anthu ake za chipulumutso pokhululukidwa machimo awo,+ 1 Yohane 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu mukudziwanso kuti iye anaonekera kuti achotse machimo athu,+ ndipo mwa iye mulibe tchimo.+