Aefeso 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mogwirizana ndi iyeyo tinaikidwa kukhala odzalandira cholowa,+ pakuti anatisankhiratu mwa kufuna kwake, iye amene amayendetsa zinthu zonse mogwirizana ndi chifuniro chake.+
11 Mogwirizana ndi iyeyo tinaikidwa kukhala odzalandira cholowa,+ pakuti anatisankhiratu mwa kufuna kwake, iye amene amayendetsa zinthu zonse mogwirizana ndi chifuniro chake.+