Yona 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma anthuwo anayesetsa kuti adutse mafunde amphamvuwo ndi kukakocheza kumtunda. Koma sanakwanitse chifukwa mkunthowo unali kuwonjezeka kwambiri.+
13 Koma anthuwo anayesetsa kuti adutse mafunde amphamvuwo ndi kukakocheza kumtunda. Koma sanakwanitse chifukwa mkunthowo unali kuwonjezeka kwambiri.+