Mateyu 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chiritsani odwala,+ ukitsani anthu akufa, yeretsani akhate, tulutsani ziwanda. Munalandira kwaulere, patsani kwaulere.+
8 Chiritsani odwala,+ ukitsani anthu akufa, yeretsani akhate, tulutsani ziwanda. Munalandira kwaulere, patsani kwaulere.+