Luka 2:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Komanso, Simiyoni anadalitsa makolowo, ndipo anauza Mariya, mayi a mwanayo kuti: “Tamverani! Uyu waikidwa kuti ambiri agwe,+ ndiponso kuti ambiri adzukenso mu Isiraeli,+ ndi kuti akhale chizindikiro chimene anthu adzachitsutse+ Yohane 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mukanakhala mbali ya dziko, dziko likanakukondani monga mbali yake.+ Koma popeza simuli mbali ya dzikoli,+ koma ine ndinakusankhani kuchokera m’dziko, pa chifukwa chimenechi dziko likudana nanu.+
34 Komanso, Simiyoni anadalitsa makolowo, ndipo anauza Mariya, mayi a mwanayo kuti: “Tamverani! Uyu waikidwa kuti ambiri agwe,+ ndiponso kuti ambiri adzukenso mu Isiraeli,+ ndi kuti akhale chizindikiro chimene anthu adzachitsutse+
19 Mukanakhala mbali ya dziko, dziko likanakukondani monga mbali yake.+ Koma popeza simuli mbali ya dzikoli,+ koma ine ndinakusankhani kuchokera m’dziko, pa chifukwa chimenechi dziko likudana nanu.+