Maliko 5:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Nthawi yomweyo kamtsikanako kanadzuka ndi kuyamba kuyenda. Mwanayo anali ndi zaka 12. Pamenepo anthuwo anasangalala kwambiri.+
42 Nthawi yomweyo kamtsikanako kanadzuka ndi kuyamba kuyenda. Mwanayo anali ndi zaka 12. Pamenepo anthuwo anasangalala kwambiri.+