Yohane 7:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Pamenepa anali kunena za mzimu umene onse okhulupirira mwa iye anali pafupi kulandira. Pakuti pa nthawiyi n’kuti asanaulandire,+ chifukwa Yesu anali asanalandire ulemerero wake.+ Afilipi 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pa chifukwa chimenechinso, Mulungu anamukweza n’kumuika pamalo apamwamba.+ Ndipo anamukomera mtima n’kumupatsa dzina loposa lina lililonse.+
39 Pamenepa anali kunena za mzimu umene onse okhulupirira mwa iye anali pafupi kulandira. Pakuti pa nthawiyi n’kuti asanaulandire,+ chifukwa Yesu anali asanalandire ulemerero wake.+
9 Pa chifukwa chimenechinso, Mulungu anamukweza n’kumuika pamalo apamwamba.+ Ndipo anamukomera mtima n’kumupatsa dzina loposa lina lililonse.+