Mateyu 27:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pamenepo bwanamkubwayo anawafunsa kuti: “Ndani mwa awiriwa amene mukufuna kuti ndikumasulireni?” Iwo anati: “Baraba.”+ Luka 23:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 ndi kuwauza kuti: “Inu mwabweretsa munthu uyu kwa ine monga wolimbikitsa anthu kuukira. Koma mwaona nokha pano! Inetu ndamufunsa pamaso panu, ndipo sindinamupeze ndi chifukwa+ chomuimbira milandu imene mukumunenezayi.
21 Pamenepo bwanamkubwayo anawafunsa kuti: “Ndani mwa awiriwa amene mukufuna kuti ndikumasulireni?” Iwo anati: “Baraba.”+
14 ndi kuwauza kuti: “Inu mwabweretsa munthu uyu kwa ine monga wolimbikitsa anthu kuukira. Koma mwaona nokha pano! Inetu ndamufunsa pamaso panu, ndipo sindinamupeze ndi chifukwa+ chomuimbira milandu imene mukumunenezayi.