Mateyu 21:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Tsopano Yesu analowa m’kachisi, ndipo pamene anali kuphunzitsa, ansembe aakulu ndiponso akulu anabwera kwa iye ndi kumufunsa kuti:+ “Kodi muli ndi ulamuliro wochitira zinthu zimenezi? Ndipo ndani anakupatsani ulamuliro umenewu?”+ Maliko 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Iwo anayamba kum’funsa kuti: “Kodi muli ndi ulamuliro wochitira zinthu zimenezi? Kapena ndani anakupatsani ulamuliro umenewu?”+ Luka 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwo anamufunsa kuti: “Tiuzeni, kodi muli ndi ulamuliro wochitira zinthu zimenezi? Kapena ndani amene anakupatsani ulamuliro umenewu?”+
23 Tsopano Yesu analowa m’kachisi, ndipo pamene anali kuphunzitsa, ansembe aakulu ndiponso akulu anabwera kwa iye ndi kumufunsa kuti:+ “Kodi muli ndi ulamuliro wochitira zinthu zimenezi? Ndipo ndani anakupatsani ulamuliro umenewu?”+
28 Iwo anayamba kum’funsa kuti: “Kodi muli ndi ulamuliro wochitira zinthu zimenezi? Kapena ndani anakupatsani ulamuliro umenewu?”+
2 Iwo anamufunsa kuti: “Tiuzeni, kodi muli ndi ulamuliro wochitira zinthu zimenezi? Kapena ndani amene anakupatsani ulamuliro umenewu?”+