Machitidwe 5:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Pamenepo iwo anamvera mawu ake, ndipo anaitanitsa atumwiwo. Ndiyeno anangowakwapula+ ndi kuwalamula kuti asiye kulankhula m’dzina la Yesu,+ kenako anawamasula.
40 Pamenepo iwo anamvera mawu ake, ndipo anaitanitsa atumwiwo. Ndiyeno anangowakwapula+ ndi kuwalamula kuti asiye kulankhula m’dzina la Yesu,+ kenako anawamasula.