Machitidwe 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ataganizira zimene zinachitikazo, iye anapita kunyumba ya Mariya, mayi wake wa Yohane wotchedwanso Maliko.+ Kumeneko anthu ambiri anali atasonkhana pamodzi ndipo anali kupemphera.
12 Ataganizira zimene zinachitikazo, iye anapita kunyumba ya Mariya, mayi wake wa Yohane wotchedwanso Maliko.+ Kumeneko anthu ambiri anali atasonkhana pamodzi ndipo anali kupemphera.