-
Machitidwe 3:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Choncho mwa chikhulupiriro chathu m’dzina lake, dzina lakelo lalimbitsa mwamunayu amene mukumuona ndi kumudziwa. Ndipo chikhulupiriro chimene ife tili nacho chifukwa cha iye chamuchiritsiratu, monga mmene nonsenu mukuonera.
-