Machitidwe 11:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mpingo wa ku Yerusalemu unamva za iwo, ndipo unatumiza Baranaba+ kuti apite ku Antiokeya. Machitidwe 12:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Tsopano Baranaba+ ndi Saulo atamaliza utumiki wopereka thandizo+ ku Yerusalemu, anabwerera ndi kutenga Yohane,+ wotchedwanso Maliko.
25 Tsopano Baranaba+ ndi Saulo atamaliza utumiki wopereka thandizo+ ku Yerusalemu, anabwerera ndi kutenga Yohane,+ wotchedwanso Maliko.