Miyambo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Uzilemekeza Yehova ndi zinthu zako zamtengo wapatali+ ndiponso ndi zipatso zako zonse zoyambirira.+ Luka 12:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Gulitsani+ zinthu zanu ndi kupereka mphatso zachifundo.+ Dzipangireni zikwama za ndalama zomwe sizingathe, kutanthauza chuma chosatha kumwamba,+ kumene mbala singafikeko, ndipo njenjete* singawononge.
9 Uzilemekeza Yehova ndi zinthu zako zamtengo wapatali+ ndiponso ndi zipatso zako zonse zoyambirira.+
33 Gulitsani+ zinthu zanu ndi kupereka mphatso zachifundo.+ Dzipangireni zikwama za ndalama zomwe sizingathe, kutanthauza chuma chosatha kumwamba,+ kumene mbala singafikeko, ndipo njenjete* singawononge.