Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 26:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pamenepo ansembe ndi aneneri anayamba kuuza akalongawo ndi anthu onse kuti: “Munthu uyu akuyenera chiweruzo cha imfa+ chifukwa chakuti wanenera za mzinda uwu monga mmene mwamvera ndi makutu anu.”+

  • Machitidwe 21:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Iwo anali kufuula kuti: “Inu Aisiraeli, tithandizeni! Munthu amene akuphunzitsa zotsutsana ndi anthu a mtundu wathu kulikonse ndi ameneyu.+ Iyeyu akuphunzitsa zotsutsana ndi Chilamulo komanso malo ano. Kuwonjezera pamenepo, inu mukudziwa kuti anatenga Agiriki n’kudzawalowetsa m’kachisi ndipo waipitsa malo oyera ano.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena