Machitidwe 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Saulo anali kuvomereza za kupha Sitefano.+ Tsiku limenelo, panabuka chizunzo chachikulu+ choukira mpingo umene unali mu Yerusalemu. Onse anabalalikira+ m’zigawo za Yudeya ndi Samariya, kupatulapo atumwi okha. Machitidwe 22:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Komanso pamene magazi a Sitefano+ mboni yanu anali kukhetsedwa, ine ndinali kuonerera ndi kuvomereza zimenezo.+ Ndinenso amene ndinali kuyang’anira malaya akunja a anthu amene anali kumuphawo.’
8 Ndiyeno Saulo anali kuvomereza za kupha Sitefano.+ Tsiku limenelo, panabuka chizunzo chachikulu+ choukira mpingo umene unali mu Yerusalemu. Onse anabalalikira+ m’zigawo za Yudeya ndi Samariya, kupatulapo atumwi okha.
20 Komanso pamene magazi a Sitefano+ mboni yanu anali kukhetsedwa, ine ndinali kuonerera ndi kuvomereza zimenezo.+ Ndinenso amene ndinali kuyang’anira malaya akunja a anthu amene anali kumuphawo.’