Genesis 50:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako anafika pamalo opunthira mbewu+ a Atadi m’chigawo cha Yorodano.+ Kumeneko, anthuwo analira ndi kubuma kwakukulu, ndipo Yosefe anachita nawo miyambo yolirira maliro a bambo ake kwa masiku 7.+
10 Kenako anafika pamalo opunthira mbewu+ a Atadi m’chigawo cha Yorodano.+ Kumeneko, anthuwo analira ndi kubuma kwakukulu, ndipo Yosefe anachita nawo miyambo yolirira maliro a bambo ake kwa masiku 7.+