Mateyu 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chotero anaitana ophunzira ake 12 aja ndi kuwapatsa ulamuliro pa mizimu yonyansa,+ kuti athe kuitulutsa ndi kuchiritsa matenda a mtundu uliwonse ndi zofooka zilizonse. Maliko 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako anaitana ophunzira 12 aja, ndipo anayamba kuwatumiza awiriawiri,+ ndi kuwapatsa mphamvu pa mizimu yonyansa.+
10 Chotero anaitana ophunzira ake 12 aja ndi kuwapatsa ulamuliro pa mizimu yonyansa,+ kuti athe kuitulutsa ndi kuchiritsa matenda a mtundu uliwonse ndi zofooka zilizonse.
7 Kenako anaitana ophunzira 12 aja, ndipo anayamba kuwatumiza awiriawiri,+ ndi kuwapatsa mphamvu pa mizimu yonyansa.+