-
Machitidwe 9:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Kumeneko anapeza munthu wina dzina lake Eneya. Popeza kuti anali wakufa ziwalo, anakhala ali chigonere pabedi lake kwa zaka 8.
-