Mateyu 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ine ndidzakupatsa makiyi a ufumu wakumwamba. Chilichonse chimene udzamanga padziko lapansi chidzakhala chitamangidwa kumwamba, ndipo chilichonse chimene udzamasula padziko lapansi chidzakhala chitamasulidwa kumwamba.”+
19 Ine ndidzakupatsa makiyi a ufumu wakumwamba. Chilichonse chimene udzamanga padziko lapansi chidzakhala chitamangidwa kumwamba, ndipo chilichonse chimene udzamasula padziko lapansi chidzakhala chitamasulidwa kumwamba.”+