Aheberi 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pochita zimenezo, muonetsetse kuti wina asalandidwe kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu,+ komanso kuti pakati panu pasatuluke muzu wapoizoni+ woyambitsa mavuto, ndi kuti ambiri asaipitsidwe nawo.+
15 Pochita zimenezo, muonetsetse kuti wina asalandidwe kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu,+ komanso kuti pakati panu pasatuluke muzu wapoizoni+ woyambitsa mavuto, ndi kuti ambiri asaipitsidwe nawo.+