Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 11:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Kenako Baranaba anapita ku Tariso+ kukafufuza Saulo+

  • Machitidwe 21:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Pamenepo Paulo ananena kuti: “Inetu ndine Myuda+ wa ku Tariso,+ ku Kilikiya, nzika ya mzinda wotchuka. Chonde ndikukupemphani, kuti mundilole ndilankhule kwa anthuwa.”

  • Machitidwe 22:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Inetu ndine Myuda,+ wobadwira ku Tariso wa ku Kilikiya,+ koma ndinaphunzitsidwa ndi Gamaliyeli+ mumzinda womwe uno. Anandiphunzitsa kutsatira Chilamulo cha makolo athu mokhwimitsa zinthu kwambiri.+ Ndipo ndinali wodzipereka+ potumikira Mulungu monga mmene nonsenu mulili lero.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena