Agalatiya 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 kuulula za Mwana wake kudzera mwa ine,+ kuti ndilengeze kwa anthu a mitundu ina uthenga wabwino wonena za iye.+ Sindinapite kukakambirana ndi anthu a thupi la nyama ndi magazi nthawi yomweyo.+
16 kuulula za Mwana wake kudzera mwa ine,+ kuti ndilengeze kwa anthu a mitundu ina uthenga wabwino wonena za iye.+ Sindinapite kukakambirana ndi anthu a thupi la nyama ndi magazi nthawi yomweyo.+