Machitidwe 11:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kenako Baranaba anapita ku Tariso+ kukafufuza Saulo+ Agalatiya 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako ndinalowa+ m’madera a Siriya ndi Kilikiya.