Machitidwe 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Saulo anali kuvomereza za kupha Sitefano.+ Tsiku limenelo, panabuka chizunzo chachikulu+ choukira mpingo umene unali mu Yerusalemu. Onse anabalalikira+ m’zigawo za Yudeya ndi Samariya, kupatulapo atumwi okha.
8 Ndiyeno Saulo anali kuvomereza za kupha Sitefano.+ Tsiku limenelo, panabuka chizunzo chachikulu+ choukira mpingo umene unali mu Yerusalemu. Onse anabalalikira+ m’zigawo za Yudeya ndi Samariya, kupatulapo atumwi okha.