Yohane 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Inenso ndidzapempha Atate, ndipo adzakupatsani mthandizi wina kuti adzakhale nanu kosatha.+