Machitidwe 9:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Tsopano pamene Petulo anali kuyendayenda m’madera onse, anafikanso kwa oyera amene anali kukhala ku Luda.+
32 Tsopano pamene Petulo anali kuyendayenda m’madera onse, anafikanso kwa oyera amene anali kukhala ku Luda.+