Luka 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 chifukwa amakonda anthu amtundu wathu+ ndipo anatimangira sunagoge.” Machitidwe 8:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ulibe gawo kapena mbali mu ntchito imeneyi, pakuti mtima wako si wowongoka pamaso pa Mulungu.+