Machitidwe 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mu Damasiko munali wophunzira wina dzina lake Hananiya.+ Ndiyeno Ambuye analankhula naye m’masomphenya kuti: “Hananiya!” Iye anayankha kuti: “Ine, Ambuye.”
10 Mu Damasiko munali wophunzira wina dzina lake Hananiya.+ Ndiyeno Ambuye analankhula naye m’masomphenya kuti: “Hananiya!” Iye anayankha kuti: “Ine, Ambuye.”