Salimo 65:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu Wakumva pemphero, anthu a mitundu yonse adzabwera kwa inu.+ Miyambo 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nsembe ya anthu oipa imam’nyansa Yehova,+ koma pemphero la anthu owongoka mtima limam’sangalatsa.+