Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 15:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Yehova amakhala kutali ndi anthu oipa,+ koma amamva pemphero la anthu olungama.+

  • Danieli 10:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pamenepo iye anandiuza kuti: “Iwe Danieli, usaope,+ pakuti kuyambira tsiku loyamba pamene unatsegula mtima wako kuti umvetse tanthauzo la zinthu zimenezi,+ ndiponso pamene unadzichepetsa pamaso pa Mulungu wako,+ mawu ako akhala akumveka ndipo ine ndabwera chifukwa cha mawu akowo.+

  • Yohane 9:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Tikudziwa kuti Mulungu samvetsera ochimwa,+ koma ngati munthu ali woopa Mulungu ndipo amachita chifuniro chake, ameneyo amamumvetsera.+

  • 1 Petulo 3:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pakuti maso+ a Yehova* ali pa olungama, ndipo makutu ake amamva pembedzero lawo,+ koma nkhope ya Yehova imakwiyira anthu ochita zoipa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena