Machitidwe 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chotero mzimu+ unandiuza kuti ndipite nawo, ndisakayikire ngakhale pang’ono. Pamenepo abale 6 awa anatsagana nane, ndipo tinakalowa m’nyumba ya munthuyo.+
12 Chotero mzimu+ unandiuza kuti ndipite nawo, ndisakayikire ngakhale pang’ono. Pamenepo abale 6 awa anatsagana nane, ndipo tinakalowa m’nyumba ya munthuyo.+