Machitidwe 9:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Kwa masiku angapo Petulo anakhalabe mu Yopa+ kwa munthu wina wofufuta zikopa, dzina lake Simoni.+