Aroma 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pajatu akumva chabe chilamulo si amene amakhala olungama pamaso pa Mulungu, koma otsatira+ chilamulo ndiwo adzayesedwa olungama.+ 1 Akorinto 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti ndi mzimu umodzi, tonsefe tinabatizidwa+ kukhala thupi limodzi, kaya tikhale Ayuda kapena Agiriki, akapolo kapena mfulu, ndipo tonsefe tinamwetsedwa+ mzimu umodzi. Agalatiya 3:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Palibe Myuda kapena Mgiriki,+ palibe kapolo kapena mfulu,+ palibenso mwamuna kapena mkazi.+ Nonsenu ndinu munthu mmodzi mwa Khristu Yesu.+
13 Pajatu akumva chabe chilamulo si amene amakhala olungama pamaso pa Mulungu, koma otsatira+ chilamulo ndiwo adzayesedwa olungama.+
13 Pakuti ndi mzimu umodzi, tonsefe tinabatizidwa+ kukhala thupi limodzi, kaya tikhale Ayuda kapena Agiriki, akapolo kapena mfulu, ndipo tonsefe tinamwetsedwa+ mzimu umodzi.
28 Palibe Myuda kapena Mgiriki,+ palibe kapolo kapena mfulu,+ palibenso mwamuna kapena mkazi.+ Nonsenu ndinu munthu mmodzi mwa Khristu Yesu.+