Luka 24:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Tsopano atakhala pansi n’kumadya nawo chakudya, anatenga mkate ndipo anaudalitsa, kuunyemanyema ndi kuwagawira.+ Yohane 21:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yesu anapita kukatenga mkate ndi kuwagawira,+ chimodzimodzinso ndi nsomba.
30 Tsopano atakhala pansi n’kumadya nawo chakudya, anatenga mkate ndipo anaudalitsa, kuunyemanyema ndi kuwagawira.+