Mateyu 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ine ndidzakupatsa makiyi a ufumu wakumwamba. Chilichonse chimene udzamanga padziko lapansi chidzakhala chitamangidwa kumwamba, ndipo chilichonse chimene udzamasula padziko lapansi chidzakhala chitamasulidwa kumwamba.”+ Machitidwe 2:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Petulo anawayankha kuti: “Lapani,+ ndipo aliyense wa inu abatizidwe+ m’dzina+ la Yesu Khristu kuti machimo anu akhululukidwe.+ Mukatero mudzalandira mphatso yaulere+ ya mzimu woyera. Machitidwe 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Atamva zimenezi, anthuwo anabatizidwa m’dzina la Ambuye Yesu.+
19 Ine ndidzakupatsa makiyi a ufumu wakumwamba. Chilichonse chimene udzamanga padziko lapansi chidzakhala chitamangidwa kumwamba, ndipo chilichonse chimene udzamasula padziko lapansi chidzakhala chitamasulidwa kumwamba.”+
38 Petulo anawayankha kuti: “Lapani,+ ndipo aliyense wa inu abatizidwe+ m’dzina+ la Yesu Khristu kuti machimo anu akhululukidwe.+ Mukatero mudzalandira mphatso yaulere+ ya mzimu woyera.