Luka 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Koma zonsezi zisanachitike, anthu adzakugwirani ndi kukuzunzani,+ adzakuperekani kumasunagoge ndi kundende. Adzakutengerani kwa mafumu ndi abwanamkubwa chifukwa cha dzina langa.+ Machitidwe 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 ndi kugwira atumwiwo n’kuwatsekera m’ndende.+
12 “Koma zonsezi zisanachitike, anthu adzakugwirani ndi kukuzunzani,+ adzakuperekani kumasunagoge ndi kundende. Adzakutengerani kwa mafumu ndi abwanamkubwa chifukwa cha dzina langa.+