2 Mbiri 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Afilisiti anali kubweretsa+ mphatso ndi ndalama kwa Yehosafati monga msonkho.+ Aluya+ nawonso anali kum’bweretsera ziweto. Ankabweretsa nkhosa zamphongo 7,700 ndi mbuzi zamphongo 7,700.+
11 Afilisiti anali kubweretsa+ mphatso ndi ndalama kwa Yehosafati monga msonkho.+ Aluya+ nawonso anali kum’bweretsera ziweto. Ankabweretsa nkhosa zamphongo 7,700 ndi mbuzi zamphongo 7,700.+