-
Machitidwe 26:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Koma Paulo anati: “Wolemekezeka a Fesito, inetu sindinachite misala ayi, koma ndikulankhula mawu a choonadi ndiponso anzeru.
-