Machitidwe 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho atumwiwo anapitiriza kuchita zizindikiro ndi zodabwitsa zambiri pakati pa anthu.+ Ndipo okhulupirira onse mogwirizana anali kusonkhana m’khonde la zipilala la Solomo.+ Machitidwe 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mulungu anapitiriza kuchita ntchito zamphamvu zodabwitsa kudzera mwa Paulo.+ Aheberi 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mulungu nayenso anachitira umboni za chipulumutsocho ndi zizindikiro, zinthu zodabwitsa, ntchito zamphamvu zosiyanasiyana+ komanso mwa kupereka mphatso zosiyanasiyana+ za mzimu woyera malinga ndi chifuniro chake.+
12 Choncho atumwiwo anapitiriza kuchita zizindikiro ndi zodabwitsa zambiri pakati pa anthu.+ Ndipo okhulupirira onse mogwirizana anali kusonkhana m’khonde la zipilala la Solomo.+
4 Mulungu nayenso anachitira umboni za chipulumutsocho ndi zizindikiro, zinthu zodabwitsa, ntchito zamphamvu zosiyanasiyana+ komanso mwa kupereka mphatso zosiyanasiyana+ za mzimu woyera malinga ndi chifuniro chake.+