Yoweli 2:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “Ndidzachita zodabwitsa kuthambo+ ndi padziko lapansi. Ndidzachititsa kuti pakhale magazi, moto ndi utsi wokwera kumwamba.+
30 “Ndidzachita zodabwitsa kuthambo+ ndi padziko lapansi. Ndidzachititsa kuti pakhale magazi, moto ndi utsi wokwera kumwamba.+