Mateyu 9:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Yesu atalowa m’nyumba, anthu akhunguwo anabwera kwa iye, ndipo anawafunsa kuti: “Kodi muli ndi chikhulupiriro+ kuti ndingachite zimenezi?” Iwo anamuyankha kuti: “Inde, Ambuye.”
28 Yesu atalowa m’nyumba, anthu akhunguwo anabwera kwa iye, ndipo anawafunsa kuti: “Kodi muli ndi chikhulupiriro+ kuti ndingachite zimenezi?” Iwo anamuyankha kuti: “Inde, Ambuye.”