Machitidwe 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthu osonkhanawo atamva mawu ake anayamba kufuula kuti: “Amenewa ndi mawu a mulungu, osati a munthu ayi!”+ Machitidwe 28:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iwo anali kuyembekezera kuti atupa kapena agwa mwadzidzidzi n’kufa. Koma atayembekezera nthawi yaitali n’kuona kuti palibe choopsa chimene chikumuchitikira, anasintha maganizo awo ndi kuyamba kumunena kuti ndi mulungu.+
22 Anthu osonkhanawo atamva mawu ake anayamba kufuula kuti: “Amenewa ndi mawu a mulungu, osati a munthu ayi!”+
6 Iwo anali kuyembekezera kuti atupa kapena agwa mwadzidzidzi n’kufa. Koma atayembekezera nthawi yaitali n’kuona kuti palibe choopsa chimene chikumuchitikira, anasintha maganizo awo ndi kuyamba kumunena kuti ndi mulungu.+