Danieli 2:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Pamenepo Mfumu Nebukadinezara anagwada ndi kuwerama mpaka nkhope yake pansi, ndipo anapereka ulemu kwa Danieli. Iye analamulanso kuti Danieli apatsidwe mphatso ndipo amufukizire zofukiza zonunkhira.+
46 Pamenepo Mfumu Nebukadinezara anagwada ndi kuwerama mpaka nkhope yake pansi, ndipo anapereka ulemu kwa Danieli. Iye analamulanso kuti Danieli apatsidwe mphatso ndipo amufukizire zofukiza zonunkhira.+