Machitidwe 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano amunawo, pamodzi ndi Paulo, anayamba ulendo wa panyanja kuchoka ku Pafo, ndipo anafika ku Pega, ku Pamfuliya.+ Koma Yohane+ anawasiya ndi kubwerera+ ku Yerusalemu.
13 Tsopano amunawo, pamodzi ndi Paulo, anayamba ulendo wa panyanja kuchoka ku Pafo, ndipo anafika ku Pega, ku Pamfuliya.+ Koma Yohane+ anawasiya ndi kubwerera+ ku Yerusalemu.